Genesis 18:22 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 22 Kenako amunawo anachoka pamalowo nʼkulowera ku Sodomu, koma Yehova+ anatsala ndi Abulahamu. Genesis Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 18:22 Kuyankha Mafunso a M’Baibulo, Nsanja ya Olonda,5/15/1988, ptsa. 21-23