-
Genesis 18:24Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
24 Bwanji ngati mumzindamo mutapezeka anthu olungama 50? Kodi muwawonongabe, osakhululukira mzindawo chifukwa cha olungama 50 amenewo?
-