Genesis 18:30 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 30 Iye anapitiriza kuti: “Chonde Yehova, musandipsere mtima,+ koma ndiloleni ndilankhulebe. Nanga atapezeka 30 okha?” Iye anayankha kuti: “Sindiwononga ndikapezamo 30.” Genesis Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 18:30 Yandikirani, ptsa. 203-204
30 Iye anapitiriza kuti: “Chonde Yehova, musandipsere mtima,+ koma ndiloleni ndilankhulebe. Nanga atapezeka 30 okha?” Iye anayankha kuti: “Sindiwononga ndikapezamo 30.”