-
Genesis 18:32Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
32 Pomaliza anati: “Pepanitu Yehova, musandipsere mtima, ndiloleni ndilankhule komaliza kokha. Nanga mutapezeka 10 okha?” Iye anayankha kuti: “Sindiwononga mzindawo chifukwa cha 10 amenewo.”
-