-
Genesis 19:2Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
2 Ndiyeno anati: “Chonde ambuye anga, tiyeni kunyumba ya kapolo wanu. Tikakusambitseni mapazi ndiponso mukagone, kuti mawa mulawirire nʼkupitiriza ulendo wanu.” Koma iwo anati: “Ayi, ife tigona mʼbwalo lamumzindawu usiku wa lero.”
-