-
Genesis 19:9Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
9 Koma iwo anati: “Choka apa!” Ananenanso kuti: “Iwe ndi wobwera kwathu kuno, ndipo ukukhala monga mlendo. Ndiye lero uzitiuza zochita? Tsopano iweyo tikuchita zoopsa kuposa iwowo.” Atatero iwo anamupanikiza kwambiri Loti, moti anatsala pangʼono kuthyola chitseko.
-