-
Genesis 19:12Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
12 Ndiyeno alendowo anafunsa Loti kuti: “Kodi uli ndi achibale alionse kuno? Uwatulutse mumzinda uno, kaya ndi akamwini ako, ana ako aamuna, ana ako aakazi kapena aliyense amene ndi mʼbale wako.
-