Genesis 19:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Malo ano tiwawononga chifukwa Yehova wamva madandaulo ambiri okhudza anthuwa,+ moti Yehova watituma kudzawononga mzindawu.”
13 Malo ano tiwawononga chifukwa Yehova wamva madandaulo ambiri okhudza anthuwa,+ moti Yehova watituma kudzawononga mzindawu.”