Genesis 19:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Atafika nawo kunja kwa mzinda, anawauza kuti: “Thawani mupulumutse moyo wanu! Musayangʼane kumbuyo+ komanso musaime pamalo alionse mʼchigawochi.+ Thawirani kudera lakumapiri kuti musaphedwe!”
17 Atafika nawo kunja kwa mzinda, anawauza kuti: “Thawani mupulumutse moyo wanu! Musayangʼane kumbuyo+ komanso musaime pamalo alionse mʼchigawochi.+ Thawirani kudera lakumapiri kuti musaphedwe!”