Genesis 19:24 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 24 Kenako Yehova anagwetsa sulufule ndi moto ngati mvula ku Sodomu ndi Gomora. Sulufule ndi motowo zinachokera kwa Yehova kumwamba.+
24 Kenako Yehova anagwetsa sulufule ndi moto ngati mvula ku Sodomu ndi Gomora. Sulufule ndi motowo zinachokera kwa Yehova kumwamba.+