Genesis 19:25 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 25 Choncho anawononga mizindayi. Anawononga chigawo chonsecho, kuphatikizapo anthu onse okhala mʼmizindayi komanso zomera zapanthaka.+
25 Choncho anawononga mizindayi. Anawononga chigawo chonsecho, kuphatikizapo anthu onse okhala mʼmizindayi komanso zomera zapanthaka.+