Genesis 19:26 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 26 Koma mkazi wa Loti amene anali kumbuyo kwake, anayangʼana kumbuyo, ndipo anasanduka chipilala chamchere.+ Genesis Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 19:26 Nsanja ya Olonda,4/15/1990, ptsa. 18-196/15/1989, tsa. 9
26 Koma mkazi wa Loti amene anali kumbuyo kwake, anayangʼana kumbuyo, ndipo anasanduka chipilala chamchere.+