Genesis 19:29 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 29 Koma Mulungu sanaiwale zimene anauza Abulahamu. Choncho pamene ankawononga mizinda ya mʼchigawocho, anatulutsa Loti mʼmizinda imeneyo. Imeneyi ndi mizinda imene Loti ankakhalako.+
29 Koma Mulungu sanaiwale zimene anauza Abulahamu. Choncho pamene ankawononga mizinda ya mʼchigawocho, anatulutsa Loti mʼmizinda imeneyo. Imeneyi ndi mizinda imene Loti ankakhalako.+