Genesis 19:38 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 38 Mwana wamngʼono nayenso anabereka mwana wamwamuna nʼkumupatsa dzina lakuti Beni-ami. Iye ndi tate wa Aamoni+ amasiku ano.
38 Mwana wamngʼono nayenso anabereka mwana wamwamuna nʼkumupatsa dzina lakuti Beni-ami. Iye ndi tate wa Aamoni+ amasiku ano.