Genesis 20:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 20 Tsopano Abulahamu anasamutsa msasa wake+ nʼkupita kudziko la Negebu ndipo anayamba kukhala pakati pa Kadesi+ ndi Shura.+ Pamene ankakhala* ku Gerari,+
20 Tsopano Abulahamu anasamutsa msasa wake+ nʼkupita kudziko la Negebu ndipo anayamba kukhala pakati pa Kadesi+ ndi Shura.+ Pamene ankakhala* ku Gerari,+