Genesis 20:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Koma Abimeleki anali asanagone ndi Sara. Choncho iye anati: “Yehova, kodi muwononga mtundu womwe ndi wosalakwa?*
4 Koma Abimeleki anali asanagone ndi Sara. Choncho iye anati: “Yehova, kodi muwononga mtundu womwe ndi wosalakwa?*