-
Genesis 20:5Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
5 Kodi mwamunayu sanandiuze yekha kuti, ‘Uyu ndi mchemwali wangaʼ? Ndipo kodi mkaziyunso sananene yekha kuti, ‘Uyu ndi mchimwene wangaʼ? Zimenezitu ndachita popanda mtima wanga kunditsutsa, komanso mosadziwa kuti ndikulakwa.”
-