-
Genesis 20:6Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
6 Kenako Mulungu woona anamuuza mʼmalotomo kuti: “Inenso ndinadziwa kuti mtima wako sunakutsutse pochita zimenezi, ndipo ndinakutchinga kuti usandichimwire. Ndiye chifukwa chake sindinakulole kuti umukhudze mkaziyu.
-