Genesis 20:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Tsopano bweza mkaziyo kwa mwamuna wake. Mwamunayo ndi mneneri,+ ndipo adzakupempherera+ moti udzakhala ndi moyo. Koma ukapanda kumubweza, udziwe kuti iweyo ndi anthu ako onse ndithu mufa.”
7 Tsopano bweza mkaziyo kwa mwamuna wake. Mwamunayo ndi mneneri,+ ndipo adzakupempherera+ moti udzakhala ndi moyo. Koma ukapanda kumubweza, udziwe kuti iweyo ndi anthu ako onse ndithu mufa.”