-
Genesis 2:21Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
21 Choncho Yehova Mulungu anagonetsa munthuyo tulo tofa nato. Munthuyo ali mʼtulo, Mulungu anamuchotsa nthiti imodzi kenako nʼkutseka pamalopo.
-