Genesis 21:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Kenako Mulungu anauza Abulahamu kuti: “Usaipidwe ndi zimene Sara akukuuza zokhudza mnyamatayo ndiponso kapolo wakoyo. Mumvere,* chifukwa mbadwa* zimene ndinakulonjeza zidzachokera mwa Isaki.+ Genesis Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 21:12 Nsanja ya Olonda,4/15/2006, ptsa. 6-7
12 Kenako Mulungu anauza Abulahamu kuti: “Usaipidwe ndi zimene Sara akukuuza zokhudza mnyamatayo ndiponso kapolo wakoyo. Mumvere,* chifukwa mbadwa* zimene ndinakulonjeza zidzachokera mwa Isaki.+