-
Genesis 21:19Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
19 Ndiyeno Mulungu anamutsegula maso Hagara, moti anaona chitsime cha madzi. Choncho anapita pachitsimecho nʼkutungira madziwo mʼthumba lachikopa lija, kenako anapatsa mnyamatayo kuti amwe.
-