Genesis 21:20 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 20 Pamene Isimaeli+ ankakula, Mulungu anakhalabe naye. Mnyamata ameneyu ankakhala mʼchipululu ndipo anakhala katswiri woponya muvi pogwiritsa ntchito uta.
20 Pamene Isimaeli+ ankakula, Mulungu anakhalabe naye. Mnyamata ameneyu ankakhala mʼchipululu ndipo anakhala katswiri woponya muvi pogwiritsa ntchito uta.