-
Genesis 21:30Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
30 Poyankha Abulahamu anati: “Mulandire ana a nkhosa aakazi 7 amene ndikukupatsaniwa, kuti akhale umboni wakuti ndinakumba chitsimechi ndine.”
-