-
Genesis 22:5Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
5 Kenako Abulahamu anauza atumiki akewo kuti: “Inu tsalani pano ndi buluyu, ine ndi mwana wangayu tikupita uko kukalambira, tikupezani.”
-