Genesis 22:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Choncho Abulahamu anatenga nkhuni zokawotchera nsembe zija nʼkumusenzetsa Isaki mwana wake ndipo iye ananyamula moto komanso mpeni.* Kenako anapitira limodzi. Genesis Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 22:6 Nsanja ya Olonda (Yophunzira),1/2017, tsa. 32
6 Choncho Abulahamu anatenga nkhuni zokawotchera nsembe zija nʼkumusenzetsa Isaki mwana wake ndipo iye ananyamula moto komanso mpeni.* Kenako anapitira limodzi.