-
Genesis 22:13Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
13 Zitatero Abulahamu anakweza maso ake nʼkuona nkhosa yamphongo chapoteropo, nyanga zake zitakodwa mʼziyangoyango. Ndiyeno Abulahamu anakaitenga nʼkuipereka nsembe yopsereza mʼmalo mwa mwana wake.
-