Genesis 22:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Choncho Abulahamu anatchula malowo dzina lakuti Yehova-yire.* Nʼchifukwa chake mpaka lero pali mawu akuti: “Mʼphiri lake Yehova adzapereka zinthu zofunikira.”+ Genesis Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 22:14 Kuyankha Mafunso a M’Baibulo,
14 Choncho Abulahamu anatchula malowo dzina lakuti Yehova-yire.* Nʼchifukwa chake mpaka lero pali mawu akuti: “Mʼphiri lake Yehova adzapereka zinthu zofunikira.”+