Genesis 22:24 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 24 Mdzakazi* wa Nahori, dzina lake Reuma anamuberekeranso ana awa: Teba, Gahamu, Tahasi ndi Maaka.