Genesis 23:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 23 Sara anakhala ndi moyo zaka 127. Zaka zimene Sara anakhala ndi moyo ndi zimenezi.+