-
Genesis 23:13Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
13 Kenako iye anauza Efuroni pamaso pa eni dzikowo kuti: “Ndimvere chonde. Ine ndikupatsa ndalama zonse zimene ungandiuze zogulira malowo. Landira silivayu kuti ndikaike mkazi wanga kumeneko.”
-