Genesis 23:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Abulahamu anamvera Efuroni, ndipo anamuyezera siliva wokwanira mtengo umene Efuroniyo ananena pamaso pa ana a Heti. Anamuyezera siliva wolemera masekeli 400,* mogwirizana ndi muyezo umene amalonda ankauvomereza.+ Genesis Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 23:16 Nsanja ya Olonda,11/15/1986, ptsa. 16, 27-28
16 Abulahamu anamvera Efuroni, ndipo anamuyezera siliva wokwanira mtengo umene Efuroniyo ananena pamaso pa ana a Heti. Anamuyezera siliva wolemera masekeli 400,* mogwirizana ndi muyezo umene amalonda ankauvomereza.+