Genesis 24:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Asanamalize nʼkomwe kulankhula, anangoona Rabeka mwana wa Betuele+ akutuluka mumzindawo. Betuele anali mwana wa Milika,+ ndipo Milika anali mkazi wa Nahori,+ mchimwene wake wa Abulahamu. Rabekayo anali atanyamula mtsuko paphewa pake.
15 Asanamalize nʼkomwe kulankhula, anangoona Rabeka mwana wa Betuele+ akutuluka mumzindawo. Betuele anali mwana wa Milika,+ ndipo Milika anali mkazi wa Nahori,+ mchimwene wake wa Abulahamu. Rabekayo anali atanyamula mtsuko paphewa pake.