-
Genesis 24:20Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
20 Choncho, iye mwamsanga anakhuthulira madzi amene anali mumtsuko aja muchomweramo ziweto. Kenako anayamba kuthamanga mobwerezabwereza kukatunga madzi ena pachitsimepo mpaka ngamila zonse za mlendoyo zitamwa mokwanira.
-