Genesis 24:22 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 22 Ngamila zija zitamaliza kumwa, mlendoyo anatenga ndolo yagolide yovala pamphuno yolemera hafu ya sekeli,* ndi zibangili ziwiri zagolide zolemera masekeli 10 nʼkumupatsa Rabeka. Genesis Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 24:22 Nsanja ya Olonda,1/1/1997, ptsa. 30-317/1/1989, tsa. 26
22 Ngamila zija zitamaliza kumwa, mlendoyo anatenga ndolo yagolide yovala pamphuno yolemera hafu ya sekeli,* ndi zibangili ziwiri zagolide zolemera masekeli 10 nʼkumupatsa Rabeka.