-
Genesis 24:32Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
32 Munthuyo atamva zimenezo, anapita nʼkukalowa mʼnyumbamo. Kenako Labani anamasula ngamila nʼkuzipatsa chakudya. Anatenganso madzi nʼkusambitsa mapazi a mlendoyo ndi mapazi a anyamata omwe anali nawo.
-