Genesis 24:36 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 36 Ndiponso Sara mkazi wake anamuberekera mbuye wangayo mwana wamwamuna, Sarayo atakalamba.+ Mbuye wanga adzamupatsa mwanayo zonse zimene ali nazo.+
36 Ndiponso Sara mkazi wake anamuberekera mbuye wangayo mwana wamwamuna, Sarayo atakalamba.+ Mbuye wanga adzamupatsa mwanayo zonse zimene ali nazo.+