Genesis 24:45 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 45 Ndisanamalize nʼkomwe kulankhula mumtima mwanga, ndinangoona Rabeka akutuluka mumzindawu, atanyamula mtsuko wake paphewa. Iye analowa mʼchitsime nʼkuyamba kutunga madzi. Kenako ndinamupempha kuti, ‘Chonde undigaireko madzi ndimwe.’+
45 Ndisanamalize nʼkomwe kulankhula mumtima mwanga, ndinangoona Rabeka akutuluka mumzindawu, atanyamula mtsuko wake paphewa. Iye analowa mʼchitsime nʼkuyamba kutunga madzi. Kenako ndinamupempha kuti, ‘Chonde undigaireko madzi ndimwe.’+