Genesis 24:47 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 47 Atachita zimenezi ndinamufunsa kuti, ‘Kodi ndiwe mwana wa ndani?’ Iye anandiyankha kuti, ‘Ine bambo anga ndi a Betuele. Bambo awo ndi a Nahori, ndipo mayi awo ndi a Milika.’ Ndiyeno ndinamuveka ndolo pamphuno ndi zibangili mʼmikono yake.+
47 Atachita zimenezi ndinamufunsa kuti, ‘Kodi ndiwe mwana wa ndani?’ Iye anandiyankha kuti, ‘Ine bambo anga ndi a Betuele. Bambo awo ndi a Nahori, ndipo mayi awo ndi a Milika.’ Ndiyeno ndinamuveka ndolo pamphuno ndi zibangili mʼmikono yake.+