-
Genesis 24:53Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
53 Kenako mtumikiyo anayamba kutulutsa zinthu zasiliva, zagolide ndi zovala nʼkupatsa Rabeka. Anaperekanso zinthu zamtengo wapatali kwa mchimwene wake wa Rabeka ndi kwa mayi ake.
-