-
Genesis 24:54Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
54 Pambuyo pake, iye limodzi ndi anyamata ake anadya ndi kumwa, ndipo anagona komweko.
Atadzuka mʼmawa, mtumiki wa Abulahamu uja anati: “Ndiloleni ndizipita kwa mbuye wanga.”
-