Genesis 24:59 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 59 Choncho iwo analola kuti mchemwali wawo Rabeka+ ndi mlezi* wake,+ apite limodzi ndi mtumiki wa Abulahamuyo ndi anyamata ake. Genesis Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 24:59 Nsanja ya Olonda (Yogawira),No. 3 2016, tsa. 15
59 Choncho iwo analola kuti mchemwali wawo Rabeka+ ndi mlezi* wake,+ apite limodzi ndi mtumiki wa Abulahamuyo ndi anyamata ake.