Genesis 24:60 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 60 Ndiyeno iwo anadalitsa Rabeka kuti: “Iwe mchemwali wathu, ukakhale mayi wa anthu masauzande kuchulukitsa ndi masauzande 10, ndipo mbadwa* zako zikalande mizinda ya adani awo.”+ Genesis Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 24:60 Mapeto a Chivumbulutso, tsa. 151
60 Ndiyeno iwo anadalitsa Rabeka kuti: “Iwe mchemwali wathu, ukakhale mayi wa anthu masauzande kuchulukitsa ndi masauzande 10, ndipo mbadwa* zako zikalande mizinda ya adani awo.”+