-
Genesis 24:61Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
61 Kenako Rabeka ndi atumiki ake aakazi ananyamuka nʼkukwera ngamila kumapita limodzi ndi mtumiki wa Abulahamu uja. Choncho mtumikiyo anatenga Rabeka nʼkupita naye.
-