Genesis 25:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Koma Abulahamu anapereka mphatso kwa ana amene adzakazi ake anamuberekera. Kenako, iye adakali ndi moyo, anatumiza anawo Kumʼmawa, kutali ndi mwana wake Isaki.+
6 Koma Abulahamu anapereka mphatso kwa ana amene adzakazi ake anamuberekera. Kenako, iye adakali ndi moyo, anatumiza anawo Kumʼmawa, kutali ndi mwana wake Isaki.+