Genesis 25:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Kenako Abulahamu anamwalira ali wokalamba, atakhala ndi moyo wabwino, wautali komanso atakhutira ndi moyo wake ndipo anaikidwa mʼmanda ngati mmene anachitira ndi makolo ake.* Genesis Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 25:8 Nsanja ya Olonda (Yophunzira),2/2016, tsa. 12 Moyo Wokhutiritsa, tsa. 28
8 Kenako Abulahamu anamwalira ali wokalamba, atakhala ndi moyo wabwino, wautali komanso atakhutira ndi moyo wake ndipo anaikidwa mʼmanda ngati mmene anachitira ndi makolo ake.*