Genesis 25:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Malo amenewa ndi omwe Abulahamu anagula kwa ana a Heti. Abulahamu anaikidwa kumeneko ndipo nʼkomwenso Sara mkazi wake anaikidwa.+
10 Malo amenewa ndi omwe Abulahamu anagula kwa ana a Heti. Abulahamu anaikidwa kumeneko ndipo nʼkomwenso Sara mkazi wake anaikidwa.+