Genesis 25:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Abulahamu atamwalira, Mulungu anapitiriza kudalitsa Isaki+ mwana wake. Isakiyo ankakhala pafupi ndi Beere-lahai-roi.+
11 Abulahamu atamwalira, Mulungu anapitiriza kudalitsa Isaki+ mwana wake. Isakiyo ankakhala pafupi ndi Beere-lahai-roi.+