Genesis 25:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Amenewa ndi ana a Isimaeli, mayina awo ndi amenewa potengera midzi yawo komanso misasa yawo.* Anali atsogoleri okwanira 12 malinga ndi mafuko awo.+
16 Amenewa ndi ana a Isimaeli, mayina awo ndi amenewa potengera midzi yawo komanso misasa yawo.* Anali atsogoleri okwanira 12 malinga ndi mafuko awo.+