Genesis 25:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Mbadwa zake zinayamba kukhala ku Havila+ pafupi ndi Shura+ moyandikana ndi Iguputo, mpaka ku Asuri. Iwo anakhala pafupi ndi abale awo onse.*+
18 Mbadwa zake zinayamba kukhala ku Havila+ pafupi ndi Shura+ moyandikana ndi Iguputo, mpaka ku Asuri. Iwo anakhala pafupi ndi abale awo onse.*+